Salimo 50:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pakuti nyama iliyonse yakutchire ndi yanga,+Ndiponso nyama zopezeka m’mapiri 1,000.+ Salimo 51:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pakuti nsembe singakusangalatseni, chifukwa ikanakusangalatsani ndikanaipereka kwa inu.+Nsembe yopsereza yathunthu singakusangalatseni.+ Ezekieli 16:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Unali kutenganso zovala zako za nsalu yopeta n’kuphimbira zifanizirozo. Komanso unkaika mafuta anga ndi zonunkhiritsa zanga+ pamaso pa zifanizirozo.
16 Pakuti nsembe singakusangalatseni, chifukwa ikanakusangalatsani ndikanaipereka kwa inu.+Nsembe yopsereza yathunthu singakusangalatseni.+
18 Unali kutenganso zovala zako za nsalu yopeta n’kuphimbira zifanizirozo. Komanso unkaika mafuta anga ndi zonunkhiritsa zanga+ pamaso pa zifanizirozo.