Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 3:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Pomalizira pake, mfumu ya Mowabu inatenga mwana wake wamwamuna woyamba kubadwa amene akanalowa ufumu m’malo mwake, n’kumupereka+ nsembe yopsereza pakhoma. Choncho panabuka mkwiyo waukulu kwambiri wokwiyira Aisiraeli, motero iwo analeka kumenyana ndi mfumu ya Mowabu ndipo anabwerera kwawo.

  • Salimo 49:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Palibe ngakhale mmodzi wa iwo amene angathe kuwombola m’bale wake,+

      Kapena kumuperekera dipo* kwa Mulungu,

  • Ezekieli 16:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 “‘Unali kutenga ana ako aamuna ndi aakazi amene unandiberekera+ n’kumawapereka nsembe kwa mafano.+ Kodi zochita zako zauhulezo sizinakukwanire?

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena