Ekisodo 13:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Ndipatulireni mwana aliyense wamwamuna woyamba kubadwa,* wa munthu ndi wa chiweto, pakati pa ana a Isiraeli. Ameneyu ndi wanga.”+ Salimo 106:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Choncho anali kukhetsa magazi a anthu osalakwa,+Magazi a ana awo aamuna ndi a ana awo aakazi,Amene anawapereka nsembe kwa mafano a ku Kanani.+Ndipo dzikolo linaipa ndi magazi amene iwo anakhetsa.+
2 “Ndipatulireni mwana aliyense wamwamuna woyamba kubadwa,* wa munthu ndi wa chiweto, pakati pa ana a Isiraeli. Ameneyu ndi wanga.”+
38 Choncho anali kukhetsa magazi a anthu osalakwa,+Magazi a ana awo aamuna ndi a ana awo aakazi,Amene anawapereka nsembe kwa mafano a ku Kanani.+Ndipo dzikolo linaipa ndi magazi amene iwo anakhetsa.+