Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 21:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Ndipo inuyo mudzachotsa mlandu wa magazi a munthu wosalakwa pakati panu,+ chifukwa mudzakhala mutachita choyenera pamaso pa Yehova.+

  • 2 Mafumu 21:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Manase anakhetsanso magazi osalakwa ochuluka zedi,+ mpaka magaziwo anadzaza nawo Yerusalemu kuyambira koyambirira mpaka kumapeto, kuwonjezera pa tchimo lake limene anachimwitsa nalo Yuda mwa kuchita zoipa pamaso pa Yehova.+

  • Yeremiya 2:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 Komanso, pazovala zako papezeka madontho a magazi a anthu+ osauka osalakwa.+ Madontho a magaziwo sindinawapeze panyumba, ngati kuti anali kuthyola nyumbayo, koma ndawapeza pazovala zako zonse.+

  • Hoseya 12:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Efuraimu anakhumudwitsa kwambiri Mulungu.+ Magazi amene iye anakhetsa ali pa iyeyo+ ndipo Ambuye Wamkulu adzamubwezera chitonzo chake.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena