Deuteronomo 19:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Diso lako lisamumvere chisoni+ ndipo uzichotsa mlandu wa magazi a munthu wosalakwa mu Isiraeli+ kuti zinthu zikuyendere bwino.
13 Diso lako lisamumvere chisoni+ ndipo uzichotsa mlandu wa magazi a munthu wosalakwa mu Isiraeli+ kuti zinthu zikuyendere bwino.