Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 24:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 “‘Munthu aliyense amene wakantha ndi kupheratu mnzake, nayenso aziphedwa ndithu.+

  • Levitiko 24:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Wokantha ndi kupheratu chiweto cha mnzake+ azilipira,+ koma wokantha ndi kupha munthu nayenso aziphedwa.+

  • Numeri 35:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 “‘Musadetse dziko+ limene mukukhalamo, chifukwa magazi ndiwo amadetsa dziko. Ndipo dziko lodetsedwa ndi magazi silingayeretsedwe mwa njira ina, koma ndi magazi a munthu amene anakhetsa magaziyo.+

  • Deuteronomo 21:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Ndipo inuyo mudzachotsa mlandu wa magazi a munthu wosalakwa pakati panu,+ chifukwa mudzakhala mutachita choyenera pamaso pa Yehova.+

  • 2 Samueli 21:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Tsopano m’masiku a Davide kunagwa njala+ zaka zitatu zotsatizana. Choncho Davide anafunsira kwa Yehova, ndipo Yehova anamuuza kuti: “Sauli pamodzi ndi nyumba yake ali ndi mlandu wa magazi chifukwa anapha Agibeoni.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena