Numeri 35:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Musamadetse dziko limene mukukhalamo, chifukwa magazi ndi amene amadetsa dziko.+ Ndipo dziko limene ladetsedwa ndi magazi silingayeretsedwe ndi china chilichonse, kupatulapo magazi a munthu amene anakhetsa magaziyo.+ Numeri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 35:33 Nsanja ya Olonda,8/1/2004, tsa. 27
33 Musamadetse dziko limene mukukhalamo, chifukwa magazi ndi amene amadetsa dziko.+ Ndipo dziko limene ladetsedwa ndi magazi silingayeretsedwe ndi china chilichonse, kupatulapo magazi a munthu amene anakhetsa magaziyo.+