1 Samueli 15:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Poyankha Samueli anati: “Kodi Yehova amakondwera ndi nsembe zopsereza+ ndi nsembe zina kuposa kumvera mawu a Yehova? Taona! Kumvera+ kuposa nsembe,+ ndipo kumvetsera mosamala kuposa mafuta+ a nkhosa zamphongo. 1 Yohane 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tikapitiriza kusunga malamulo ake ndiye kuti tikumudziwa.+
22 Poyankha Samueli anati: “Kodi Yehova amakondwera ndi nsembe zopsereza+ ndi nsembe zina kuposa kumvera mawu a Yehova? Taona! Kumvera+ kuposa nsembe,+ ndipo kumvetsera mosamala kuposa mafuta+ a nkhosa zamphongo.