Yohane 14:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Amene ali ndi malamulo anga ndipo amawasunga, ameneyo ndiye amene amandikonda.+ Komanso wondikonda ine, Atate wanga adzamukondanso. Inenso ndidzamukonda ndipo ndidzadzionetsera bwinobwino kwa iye.” Yohane 15:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mukasunga malamulo anga,+ mudzakhalabe m’chikondi changa, monga mmene ine ndasungira malamulo a Atate+ ndi kukhalabe m’chikondi chake.
21 Amene ali ndi malamulo anga ndipo amawasunga, ameneyo ndiye amene amandikonda.+ Komanso wondikonda ine, Atate wanga adzamukondanso. Inenso ndidzamukonda ndipo ndidzadzionetsera bwinobwino kwa iye.”
10 Mukasunga malamulo anga,+ mudzakhalabe m’chikondi changa, monga mmene ine ndasungira malamulo a Atate+ ndi kukhalabe m’chikondi chake.