1 Yohane 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma aliyense wosunga mawu ake,+ amasonyeza kuti amakondadi Mulungu.+ Chifukwa cha zimenezi, timadziwa kuti ndife ogwirizana naye.+ 1 Yohane 5:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Onse amene amakhulupirira kuti Yesu ndi Khristu, ndi ana a Mulungu,+ ndipo onse amene amakonda Atate amakondanso mwana wake.+
5 Koma aliyense wosunga mawu ake,+ amasonyeza kuti amakondadi Mulungu.+ Chifukwa cha zimenezi, timadziwa kuti ndife ogwirizana naye.+
5 Onse amene amakhulupirira kuti Yesu ndi Khristu, ndi ana a Mulungu,+ ndipo onse amene amakonda Atate amakondanso mwana wake.+