Hoseya 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pakuti ndimakondwera ndi kukoma mtima kosatha,+ osati ndi nsembe.+ Ndimakondweranso ndi kudziwa Mulungu, osati ndi nsembe zopsereza zathunthu.+ Mika 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kodi nditenge chiyani popita kukakumana+ ndi Yehova? Ndikagwade ndi chiyani kwa Mulungu wakumwamba?+ Kodi ndipite nditatenga nsembe zopsereza zathunthu+ ndi ana a ng’ombe achaka chimodzi? Mateyu 9:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choncho pitani mukaphunzire tanthauzo la mawu akuti, ‘Ndikufuna chifundo, osati nsembe.’+ Chifukwa ine sindinabwere kudzaitana anthu olungama, koma ochimwa.”
6 Pakuti ndimakondwera ndi kukoma mtima kosatha,+ osati ndi nsembe.+ Ndimakondweranso ndi kudziwa Mulungu, osati ndi nsembe zopsereza zathunthu.+
6 Kodi nditenge chiyani popita kukakumana+ ndi Yehova? Ndikagwade ndi chiyani kwa Mulungu wakumwamba?+ Kodi ndipite nditatenga nsembe zopsereza zathunthu+ ndi ana a ng’ombe achaka chimodzi?
13 Choncho pitani mukaphunzire tanthauzo la mawu akuti, ‘Ndikufuna chifundo, osati nsembe.’+ Chifukwa ine sindinabwere kudzaitana anthu olungama, koma ochimwa.”