Salimo 50:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ngakhale nditakhala ndi njala, sindingakuuze,Pakuti dziko lonse+ ndiponso zonse za mmenemo ndi zanga.+ Machitidwe 17:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Komanso satumikiridwa ndi manja a anthu ngati kuti amasowa kanthu,+ chifukwa ndi iyeyo amene amapatsa anthu onse moyo,+ mpweya,+ ndi zinthu zonse.
12 Ngakhale nditakhala ndi njala, sindingakuuze,Pakuti dziko lonse+ ndiponso zonse za mmenemo ndi zanga.+
25 Komanso satumikiridwa ndi manja a anthu ngati kuti amasowa kanthu,+ chifukwa ndi iyeyo amene amapatsa anthu onse moyo,+ mpweya,+ ndi zinthu zonse.