Salimo 95:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Bwerani timuweramire ndi kumupembedza.+Tiyeni tigwade+ pamaso pa Yehova amene ndiye Wotipanga.+ Aefeso 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pa chifukwa chimenechi ndikupinda mawondo+ anga kwa Atate,+