1 Mafumu 8:54 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 54 Tsopano Solomo atangomaliza kupemphera kwa Yehova pemphero lonseli, ndi pempho lopempha chifundo, anaimirira patsogolo pa guwa lansembe la Yehova popeza nthawi yonseyi anali chogwada,+ manja ake atawatambasulira kumwamba.+ Ezara 9:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pa nthawi yopereka nsembe yambewu+ yamadzulo, pambuyo podzichepetsa mwanjira imeneyi, ndinaimirira, zovala zanga zitang’ambika, ndipo ndinagwada+ n’kutambasulira manja anga kwa Yehova Mulungu wanga.+ Aefeso 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pa chifukwa chimenechi ndikupinda mawondo+ anga kwa Atate,+
54 Tsopano Solomo atangomaliza kupemphera kwa Yehova pemphero lonseli, ndi pempho lopempha chifundo, anaimirira patsogolo pa guwa lansembe la Yehova popeza nthawi yonseyi anali chogwada,+ manja ake atawatambasulira kumwamba.+
5 Pa nthawi yopereka nsembe yambewu+ yamadzulo, pambuyo podzichepetsa mwanjira imeneyi, ndinaimirira, zovala zanga zitang’ambika, ndipo ndinagwada+ n’kutambasulira manja anga kwa Yehova Mulungu wanga.+