Ekisodo 9:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Choncho Mose anamuyankha kuti: “Ndikangotuluka mumzinda uno, ndikweza manja anga kwa Yehova.+ Mabingu ndi matalala asiya, kuti mudziwe kuti dziko lapansi ndi la Yehova.+ Salimo 143:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ine ndikupemphera nditakweza manja anga kwa inu.+Moyo wanga uli ngati dziko louma limene likulakalaka kuti muthetse ludzu lake.+ [Seʹlah.]
29 Choncho Mose anamuyankha kuti: “Ndikangotuluka mumzinda uno, ndikweza manja anga kwa Yehova.+ Mabingu ndi matalala asiya, kuti mudziwe kuti dziko lapansi ndi la Yehova.+
6 Ine ndikupemphera nditakweza manja anga kwa inu.+Moyo wanga uli ngati dziko louma limene likulakalaka kuti muthetse ludzu lake.+ [Seʹlah.]