Deuteronomo 10:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Taonani, kumwamba ndi kwa Yehova Mulungu wanu,+ kumwambamwamba ndi zonse zili kumeneko, dziko lapansi+ ndi zonse zili mmenemo ndi zake zonsezo. Salimo 24:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Dziko lapansi ndi zonse zili mmenemo ndi za Yehova,+Nthaka ndi yake pamodzi ndi onse okhala panthakapo.+ Salimo 50:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ngakhale nditakhala ndi njala, sindingakuuze,Pakuti dziko lonse+ ndiponso zonse za mmenemo ndi zanga.+ 1 Akorinto 10:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 chifukwa “dziko lapansi ndi zonse za mmenemo+ ndi za Yehova.”+
14 Taonani, kumwamba ndi kwa Yehova Mulungu wanu,+ kumwambamwamba ndi zonse zili kumeneko, dziko lapansi+ ndi zonse zili mmenemo ndi zake zonsezo.
24 Dziko lapansi ndi zonse zili mmenemo ndi za Yehova,+Nthaka ndi yake pamodzi ndi onse okhala panthakapo.+
12 Ngakhale nditakhala ndi njala, sindingakuuze,Pakuti dziko lonse+ ndiponso zonse za mmenemo ndi zanga.+