Ekisodo 19:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Tsopano ngati mudzalabadiradi+ mawu anga ndi kusunga pangano langa,+ pamenepo mudzakhaladi chuma changa chapadera pakati pa anthu ena onse,+ chifukwa dziko lonse lapansi ndi langa.+ Deuteronomo 10:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Taonani, kumwamba ndi kwa Yehova Mulungu wanu,+ kumwambamwamba ndi zonse zili kumeneko, dziko lapansi+ ndi zonse zili mmenemo ndi zake zonsezo.
5 Tsopano ngati mudzalabadiradi+ mawu anga ndi kusunga pangano langa,+ pamenepo mudzakhaladi chuma changa chapadera pakati pa anthu ena onse,+ chifukwa dziko lonse lapansi ndi langa.+
14 Taonani, kumwamba ndi kwa Yehova Mulungu wanu,+ kumwambamwamba ndi zonse zili kumeneko, dziko lapansi+ ndi zonse zili mmenemo ndi zake zonsezo.