Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 95:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Bwerani timuweramire ndi kumupembedza.+

      Tiyeni tigwade+ pamaso pa Yehova amene ndiye Wotipanga.+

  • Luka 22:41
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 41 Iye analekana nawo ndi kuyenda kamtunda, kutalika kwake ngati pamene pangagwere mwala munthu atauponya. Kumeneko anagwada ndi kuyamba kupemphera,

  • Machitidwe 21:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Choncho titatsiriza masikuwo, tinanyamuka kuti tipitirize ulendo wathu. Ndipo abale onse, pamodzi ndi amayi ndi ana, anatiperekeza mpaka kunja kwa mzindawo. Kumeneko tinagwada+ pagombe ndi kupemphera

  • Aefeso 3:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Pa chifukwa chimenechi ndikupinda mawondo+ anga kwa Atate,+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena