2 Mbiri 6:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Tsopano Solomo anaimirira patsogolo pa guwa lansembe la Yehova patsogolo pa mpingo wonse wa Isiraeli.+ Kenako anatambasula manja ake.+ Ezara 9:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pa nthawi yopereka nsembe yambewu+ yamadzulo, pambuyo podzichepetsa mwanjira imeneyi, ndinaimirira, zovala zanga zitang’ambika, ndipo ndinagwada+ n’kutambasulira manja anga kwa Yehova Mulungu wanga.+
12 Tsopano Solomo anaimirira patsogolo pa guwa lansembe la Yehova patsogolo pa mpingo wonse wa Isiraeli.+ Kenako anatambasula manja ake.+
5 Pa nthawi yopereka nsembe yambewu+ yamadzulo, pambuyo podzichepetsa mwanjira imeneyi, ndinaimirira, zovala zanga zitang’ambika, ndipo ndinagwada+ n’kutambasulira manja anga kwa Yehova Mulungu wanga.+