Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 15:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Poyankha Samueli anati: “Kodi Yehova amakondwera ndi nsembe zopsereza+ ndi nsembe zina kuposa kumvera mawu a Yehova? Taona! Kumvera+ kuposa nsembe,+ ndipo kumvetsera mosamala kuposa mafuta+ a nkhosa zamphongo.

  • Salimo 50:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Sindikukudzudzulani chifukwa cha nsembe zanu,+

      Kapena chifukwa cha nsembe zanu zopsereza zathunthu zimene mumapereka kwa ine nthawi zonse.+

  • Salimo 51:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Pakuti nsembe singakusangalatseni, chifukwa ikanakusangalatsani ndikanaipereka kwa inu.+

      Nsembe yopsereza yathunthu singakusangalatseni.+

  • Yesaya 1:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Yehova wanena kuti: “Kodi nsembe zanu zambirimbirizo zili ndi phindu lanji kwa ine? Nsembe zopsereza zathunthu+ za nkhosa zamphongo+ ndiponso mafuta a nyama zodyetsedwa bwino zandikwana.+ Ine sindikusangalalanso+ ndi magazi+ a ana a ng’ombe amphongo, ana a nkhosa amphongo ndiponso a mbuzi zamphongo.+

  • Yesaya 40:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Ngakhale mitengo yonse ya ku Lebanoni singakwane kusonkhezera moto kuti usazime, ndipo nyama zake zam’tchire+ si zokwanira kukhala nsembe yopsereza.+

  • Hoseya 6:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Pakuti ndimakondwera ndi kukoma mtima kosatha,+ osati ndi nsembe.+ Ndimakondweranso ndi kudziwa Mulungu, osati ndi nsembe zopsereza zathunthu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena