Deuteronomo 8:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mungaiwale amene anakuyendetsani m’chipululu chachikulu ndi chochititsa mantha,+ chokhala ndi njoka zapoizoni,+ zinkhanira ndiponso dziko louma lopanda madzi. Amenenso anakutulutsirani madzi pamwala wolimba ngati nsangalabwi.+ Hoseya 13:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ine ndinakudziwa uli m’chipululu,+ m’dziko la matenda otenthetsa thupi.+
15 Mungaiwale amene anakuyendetsani m’chipululu chachikulu ndi chochititsa mantha,+ chokhala ndi njoka zapoizoni,+ zinkhanira ndiponso dziko louma lopanda madzi. Amenenso anakutulutsirani madzi pamwala wolimba ngati nsangalabwi.+