Salimo 91:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Adzakuphimba ndi mapiko ake,Ndipo udzathawira pansi pa mapiko ake.*+ Kukhulupirika kwake+ kudzakhala chishango chako chachikulu+ komanso khoma lokuteteza. Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 91:4 Nsanja ya Olonda,10/1/2002, tsa. 1211/15/2001, ptsa. 16-176/15/2001, tsa. 264/15/2000, tsa. 7
4 Adzakuphimba ndi mapiko ake,Ndipo udzathawira pansi pa mapiko ake.*+ Kukhulupirika kwake+ kudzakhala chishango chako chachikulu+ komanso khoma lokuteteza.