Salimo 91:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Adzakutchinjiriza ndi mapiko ake,+Udzathawira pansi pa mapiko ake.+Choonadi chake+ chidzakhala chishango chako+ chachikulu ndi malo ako achitetezo. Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 91:4 Nsanja ya Olonda,10/1/2002, tsa. 1211/15/2001, ptsa. 16-176/15/2001, tsa. 264/15/2000, tsa. 7
4 Adzakutchinjiriza ndi mapiko ake,+Udzathawira pansi pa mapiko ake.+Choonadi chake+ chidzakhala chishango chako+ chachikulu ndi malo ako achitetezo.