Salimo 57:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Adzatumiza thandizo kuchokera kumwamba nʼkundipulumutsa.+ Adzasokoneza wofuna kundiwakha ndi pakamwa pake. (Selah) Mulungu adzasonyeza chikondi chake chokhulupirika ndi choonadi chake.+ Salimo 86:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma inu Yehova, ndinu Mulungu wachifundo komanso wokoma mtima,Wosakwiya msanga, wachikondi chokhulupirika chochuluka ndiponso wokhulupirika.*+
3 Adzatumiza thandizo kuchokera kumwamba nʼkundipulumutsa.+ Adzasokoneza wofuna kundiwakha ndi pakamwa pake. (Selah) Mulungu adzasonyeza chikondi chake chokhulupirika ndi choonadi chake.+
15 Koma inu Yehova, ndinu Mulungu wachifundo komanso wokoma mtima,Wosakwiya msanga, wachikondi chokhulupirika chochuluka ndiponso wokhulupirika.*+