Salimo 40:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Inu Yehova, musasiye kundisonyeza chifundo. Chikondi chanu chokhulupirika komanso choonadi chanu zizinditeteza nthawi zonse.+ Salimo 61:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mfumuyo idzakhala pampando wachifumu mpaka kalekale pamaso pa Mulungu.+Chikondi chanu chokhulupirika komanso kukhulupirika kwanu ziiteteze.+
11 Inu Yehova, musasiye kundisonyeza chifundo. Chikondi chanu chokhulupirika komanso choonadi chanu zizinditeteza nthawi zonse.+
7 Mfumuyo idzakhala pampando wachifumu mpaka kalekale pamaso pa Mulungu.+Chikondi chanu chokhulupirika komanso kukhulupirika kwanu ziiteteze.+