Salimo 63:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 63 Inu Mulungu, ndinu Mulungu wanga, ine ndikukufunafunani.+Moyo wanga ukulakalaka inu.+Thupi langa lalefuka chifukwa cholakalaka inuM’dziko louma ndi lopanda chonde, lopanda madzi.+ Salimo 77:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Usiku ndidzakumbukira nyimbo zanga zoimbidwa ndi chipangizo cha zingwe.+Ndidzasonyeza kudera nkhawa mumtima mwanga,+Ndipo ndidzasinkhasinkha zinthu zonse mozama.
63 Inu Mulungu, ndinu Mulungu wanga, ine ndikukufunafunani.+Moyo wanga ukulakalaka inu.+Thupi langa lalefuka chifukwa cholakalaka inuM’dziko louma ndi lopanda chonde, lopanda madzi.+
6 Usiku ndidzakumbukira nyimbo zanga zoimbidwa ndi chipangizo cha zingwe.+Ndidzasonyeza kudera nkhawa mumtima mwanga,+Ndipo ndidzasinkhasinkha zinthu zonse mozama.