Salimo 42:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Moyo wanga ukulakalaka Mulungu,+ ukulakalaka Mulungu wamoyo.+Ndidzapita liti kunyumba ya Mulungu kukaonekera pamaso pake?+ Salimo 143:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ine ndikupemphera nditakweza manja anga kwa inu.+Moyo wanga uli ngati dziko louma limene likulakalaka kuti muthetse ludzu lake.+ [Seʹlah.]
2 Moyo wanga ukulakalaka Mulungu,+ ukulakalaka Mulungu wamoyo.+Ndidzapita liti kunyumba ya Mulungu kukaonekera pamaso pake?+
6 Ine ndikupemphera nditakweza manja anga kwa inu.+Moyo wanga uli ngati dziko louma limene likulakalaka kuti muthetse ludzu lake.+ [Seʹlah.]