Salimo 63:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 63 Inu Mulungu, ndinu Mulungu wanga, ine ndikukufunafunani.+Moyo wanga ukulakalaka inu.+Thupi langa lalefuka chifukwa cholakalaka inuMādziko louma ndi lopanda chonde, lopanda madzi.+
63 Inu Mulungu, ndinu Mulungu wanga, ine ndikukufunafunani.+Moyo wanga ukulakalaka inu.+Thupi langa lalefuka chifukwa cholakalaka inuMādziko louma ndi lopanda chonde, lopanda madzi.+