Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 32:40
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 40 Ndikukweza dzanja langa kumwamba polumbira,+

      Ndipo ndikunena kuti: “Pali ine, Mulungu wamoyo wosatha,”+

  • Yoswa 3:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Atafika, Yoswa anati: “Mukaona zimene zichitike pano, mudziwa kuti Mulungu wamoyo alidi pakati panu.+ Mudziwanso kuti iye adzathamangitsadi pamaso panu Akanani, Ahiti, Ahivi, Aperezi, Agirigasi, Aamori ndi Ayebusi.+

  • Yeremiya 10:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Koma Yehova ndi Mulungu woonadi.+ Iye ndi Mulungu wamoyo+ ndipo ndi Mfumu mpaka kalekale.+ Dziko lapansi lidzagwedezeka ndi mkwiyo wake,+ ndipo palibe mitundu ya anthu imene idzalimbe pamene iye akuidzudzula.+

  • Mateyu 16:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Poyankha, Simoni Petulo ananena kuti: “Ndinu Khristu,+ Mwana wa Mulungu wamoyo.”+

  • 1 Atesalonika 1:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Pakuti iwo amanena mmene ife tinafikira pakati panu koyamba. Amanenanso mmene inu munatembenukira kwa Mulungu, kusiya mafano+ anu kuti mutumikire Mulungu wamoyo+ ndi woona,+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena