7 ndipo iye anatcha malowo Masa*+ ndi Meriba,*+ chifukwa ana a Isiraeli anakangana ndi Mose, komanso chifukwa cha kuyesa Yehova+ kuti: “Kodi pakati pathu pano, Yehova alipo kapena ayi?”+
20 koma mudzaidya kwa mwezi wonse wathunthu, mpaka idzatulukira m’mphuno mwanu, ndipo mudzachita kunyansidwa nayo.+ Zidzatero chifukwa mwakana Yehova amene ali pakati panu, ndipo mukum’lirira kuti: “Tinachokeranji ku Iguputo?”’”+