Ekisodo 17:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Choncho iye anatchula malowo kuti Masa*+ ndi Meriba,*+ chifukwa Aisiraeli anakangana ndi Mose komanso chifukwa chakuti anayesa Yehova+ kuti: “Kodi pakati pathu pano, Yehova alipo kapena ayi?”
7 Choncho iye anatchula malowo kuti Masa*+ ndi Meriba,*+ chifukwa Aisiraeli anakangana ndi Mose komanso chifukwa chakuti anayesa Yehova+ kuti: “Kodi pakati pathu pano, Yehova alipo kapena ayi?”