Ekisodo 17:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 ndipo iye anatcha malowo Masa*+ ndi Meriba,*+ chifukwa ana a Isiraeli anakangana ndi Mose, komanso chifukwa cha kuyesa Yehova+ kuti: “Kodi pakati pathu pano, Yehova alipo kapena ayi?”+
7 ndipo iye anatcha malowo Masa*+ ndi Meriba,*+ chifukwa ana a Isiraeli anakangana ndi Mose, komanso chifukwa cha kuyesa Yehova+ kuti: “Kodi pakati pathu pano, Yehova alipo kapena ayi?”+