Numeri 14:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Chongofunika n’chakuti musam’pandukire Yehova.+ Komanso anthu a m’dzikolo musawaope,+ chifukwa ali ngati chakudya kwa ife. Alibenso chitetezo,+ koma ifeyo Yehova ali nafe.+ Musawaope ayi.”+ Salimo 46:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mulungu ali pakati pa mzinda.+ Mzindawo sudzagwedezeka.+Mulungu adzauthandiza m’bandakucha.+
9 Chongofunika n’chakuti musam’pandukire Yehova.+ Komanso anthu a m’dzikolo musawaope,+ chifukwa ali ngati chakudya kwa ife. Alibenso chitetezo,+ koma ifeyo Yehova ali nafe.+ Musawaope ayi.”+