Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 48:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Isiraeli atatero, anauza Yosefe kuti: “Taona, inetu ndikufa.+ Koma Mulungu adzakhalabe nanu ndithu anthu inu, ndipo adzakubwezerani kudziko la makolo anu.+

  • Ekisodo 33:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Ndipo ndidziwa bwanji kuti mwandikomera mtima, ineyo ndi anthu anu? Si mwa kuyenda nafe kodi?+ Pajatu ine ndi anthu anu mwatisiyanitsa ndi anthu ena onse amene ali padziko lapansi.”+

  • Deuteronomo 20:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 “Mukapita kunkhondo kukamenyana ndi adani anu, musachite nawo mantha mukaona kuti ali ndi mahatchi ndi magaleta ankhondo,+ ndiponso mukaona kuti adani anuwo ndi ochuluka kwambiri kuposa inu. Yehova Mulungu wanu, amene anakutulutsani m’dziko la Iguputo ali ndi inu.+

  • Yesaya 41:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Usachite mantha, pakuti ndili nawe.+ Usayang’ane uku ndi uku mwamantha, pakuti ine ndine Mulungu wako.+ Ndikulimbitsa.+ Ndithu ndikuthandiza.+ Ndikugwira mwamphamvu ndi dzanja langa lamanja+ lachilungamo.’+

  • Aroma 8:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Ndiye tinene kuti chiyani pa zinthu zimenezi? Ngati Mulungu ali kumbali yathu, ndani adzatsutsana nafe?+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena