Genesis 50:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Potsirizira pake, Yosefe anauza abale ake kuti: “Ine ndikufa, koma Mulungu adzakucheukirani,+ ndipo adzakutulutsani ndithu m’dziko lino. Adzakupititsani kudziko limene analonjeza polumbira kwa Abulahamu, kwa Isaki ndi kwa Yakobo.”+
24 Potsirizira pake, Yosefe anauza abale ake kuti: “Ine ndikufa, koma Mulungu adzakucheukirani,+ ndipo adzakutulutsani ndithu m’dziko lino. Adzakupititsani kudziko limene analonjeza polumbira kwa Abulahamu, kwa Isaki ndi kwa Yakobo.”+