Salimo 65:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mudzatiyankha ndi zinthu zochititsa mantha zochitika mwachilungamo,+Inu Mulungu wa chipulumutso chathu,+Inu Chidaliro cha malire onse a dziko lapansi ndi anthu okhala pafupi ndi nyanja zakutali.+ Salimo 89:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Chilungamo ndi chiweruzo ndizo maziko a mpando wanu wachifumu.+Kukoma mtima kosatha ndi choonadi zili pamaso panu.+
5 Mudzatiyankha ndi zinthu zochititsa mantha zochitika mwachilungamo,+Inu Mulungu wa chipulumutso chathu,+Inu Chidaliro cha malire onse a dziko lapansi ndi anthu okhala pafupi ndi nyanja zakutali.+
14 Chilungamo ndi chiweruzo ndizo maziko a mpando wanu wachifumu.+Kukoma mtima kosatha ndi choonadi zili pamaso panu.+