Deuteronomo 32:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iye ndi Thanthwe, ndipo ntchito yake ndi yangwiro,+Njira zake zonse ndi zolungama.+Mulungu wokhulupirika,+ amene sachita chosalungama.+Iye ndi wolungama ndi wowongoka.+ Salimo 5:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pakuti inu sindinu Mulungu wokondwera ndi zoipa,+Palibe munthu woipa amene angakhale ndi inu ngakhale kwa kanthawi kochepa.+ Salimo 71:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Chilungamo chanu, inu Mulungu chafika kumwamba.+Tikanena za zinthu zazikulu zimene munachita,+Inu Mulungu, ndani angafanane ndi inu?+ Salimo 97:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mitambo ndi mdima wandiweyani zamuzungulira.+Chilungamo ndi chiweruzo ndizo malo okhazikika a mpando wake wachifumu.+ Salimo 145:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Yehova ndi wolungama m’njira zake zonse,+Ndipo ndi wokhulupirika m’ntchito zake zonse.+ Miyambo 16:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kuchita zinthu zoipa kumanyansa mafumu,+ chifukwa mpando wachifumu umakhazikika ndi chilungamo.+ Chivumbulutso 15:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iwo akuimba nyimbo ya Mose+ kapolo wa Mulungu, ndi nyimbo ya Mwanawankhosa,+ yakuti: “Ntchito zanu n’zazikulu ndi zodabwitsa,+ inu Yehova Mulungu Wamphamvuyonse.+ Njira zanu ndi zolungama ndi zoona,+ inu Mfumu yamuyaya.+
4 Iye ndi Thanthwe, ndipo ntchito yake ndi yangwiro,+Njira zake zonse ndi zolungama.+Mulungu wokhulupirika,+ amene sachita chosalungama.+Iye ndi wolungama ndi wowongoka.+
4 Pakuti inu sindinu Mulungu wokondwera ndi zoipa,+Palibe munthu woipa amene angakhale ndi inu ngakhale kwa kanthawi kochepa.+
19 Chilungamo chanu, inu Mulungu chafika kumwamba.+Tikanena za zinthu zazikulu zimene munachita,+Inu Mulungu, ndani angafanane ndi inu?+
2 Mitambo ndi mdima wandiweyani zamuzungulira.+Chilungamo ndi chiweruzo ndizo malo okhazikika a mpando wake wachifumu.+
3 Iwo akuimba nyimbo ya Mose+ kapolo wa Mulungu, ndi nyimbo ya Mwanawankhosa,+ yakuti: “Ntchito zanu n’zazikulu ndi zodabwitsa,+ inu Yehova Mulungu Wamphamvuyonse.+ Njira zanu ndi zolungama ndi zoona,+ inu Mfumu yamuyaya.+