Salimo 86:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Inu Yehova, palibe mulungu wina amene angafanane ndi inu.+Ndipo palibe ntchito zilizonse zofanana ndi ntchito zanu.+ Salimo 89:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mulungu ayenera kuopedwa pakati pa gulu lake la oyera.+Iye ndi wamkulu ndi wochititsa mantha kuposa onse omuzungulira.+
8 Inu Yehova, palibe mulungu wina amene angafanane ndi inu.+Ndipo palibe ntchito zilizonse zofanana ndi ntchito zanu.+
7 Mulungu ayenera kuopedwa pakati pa gulu lake la oyera.+Iye ndi wamkulu ndi wochititsa mantha kuposa onse omuzungulira.+