Ekisodo 15:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pa nthawiyo Mose ndi ana a Isiraeli anayamba kuimbira Yehova nyimbo iyi, kuti:+“Ndiimbira Yehova, pakuti iye wakwezeka koposa.+Waponyera m’nyanja mahatchi ndi okwera pamahatchiwo.+ Deuteronomo 31:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Chotero Mose anayamba kulankhula mawu onse a nyimbo iyi, mpingo wonse wa Isiraeli ukumva,+ ndipo anati: Aheberi 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndipo Mose monga wantchito+ anali wokhulupirika m’nyumba yonse ya Mulungu. Utumiki wakewo unali umboni wa zinthu zimene zidzalankhulidwe m’tsogolo.+
15 Pa nthawiyo Mose ndi ana a Isiraeli anayamba kuimbira Yehova nyimbo iyi, kuti:+“Ndiimbira Yehova, pakuti iye wakwezeka koposa.+Waponyera m’nyanja mahatchi ndi okwera pamahatchiwo.+
30 Chotero Mose anayamba kulankhula mawu onse a nyimbo iyi, mpingo wonse wa Isiraeli ukumva,+ ndipo anati:
5 Ndipo Mose monga wantchito+ anali wokhulupirika m’nyumba yonse ya Mulungu. Utumiki wakewo unali umboni wa zinthu zimene zidzalankhulidwe m’tsogolo.+