Oweruza 5:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pa tsiku limenelo, Debora+ ndi Baraki+ mwana wa Abinowamu,+ anayamba kuimba nyimbo,+ ndipo anati: 2 Samueli 22:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Davide analankhula ndi Yehova mawu a nyimbo iyi,+ pa tsiku limene Yehova anamulanditsa kwa adani ake+ onse ndiponso m’manja mwa Sauli.+ Chivumbulutso 15:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iwo akuimba nyimbo ya Mose+ kapolo wa Mulungu, ndi nyimbo ya Mwanawankhosa,+ yakuti: “Ntchito zanu n’zazikulu ndi zodabwitsa,+ inu Yehova Mulungu Wamphamvuyonse.+ Njira zanu ndi zolungama ndi zoona,+ inu Mfumu yamuyaya.+
5 Pa tsiku limenelo, Debora+ ndi Baraki+ mwana wa Abinowamu,+ anayamba kuimba nyimbo,+ ndipo anati: 2 Samueli 22:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Davide analankhula ndi Yehova mawu a nyimbo iyi,+ pa tsiku limene Yehova anamulanditsa kwa adani ake+ onse ndiponso m’manja mwa Sauli.+ Chivumbulutso 15:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iwo akuimba nyimbo ya Mose+ kapolo wa Mulungu, ndi nyimbo ya Mwanawankhosa,+ yakuti: “Ntchito zanu n’zazikulu ndi zodabwitsa,+ inu Yehova Mulungu Wamphamvuyonse.+ Njira zanu ndi zolungama ndi zoona,+ inu Mfumu yamuyaya.+
22 Davide analankhula ndi Yehova mawu a nyimbo iyi,+ pa tsiku limene Yehova anamulanditsa kwa adani ake+ onse ndiponso m’manja mwa Sauli.+
3 Iwo akuimba nyimbo ya Mose+ kapolo wa Mulungu, ndi nyimbo ya Mwanawankhosa,+ yakuti: “Ntchito zanu n’zazikulu ndi zodabwitsa,+ inu Yehova Mulungu Wamphamvuyonse.+ Njira zanu ndi zolungama ndi zoona,+ inu Mfumu yamuyaya.+