Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 15:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Pa nthawiyo Mose ndi ana a Isiraeli anayamba kuimbira Yehova nyimbo iyi, kuti:+

      “Ndiimbira Yehova, pakuti iye wakwezeka koposa.+

      Waponyera m’nyanja mahatchi ndi okwera pamahatchiwo.+

  • Deuteronomo 31:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 “Tsopano dzilembereni nyimbo iyi+ ndi kuwaphunzitsa ana a Isiraeli.+ Muiike m’kamwa mwawo kuti nyimbo imeneyi ikhale mboni yanga pamaso pa ana a Isiraeliwo.+

  • Deuteronomo 31:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Chotero Mose anayamba kulankhula mawu onse a nyimbo iyi, mpingo wonse wa Isiraeli ukumva,+ ndipo anati:

  • 1 Mbiri 16:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Muimbireni,+ muimbireni nyimbo zomutamanda!+

      Sinkhasinkhani ntchito zake zonse zodabwitsa.+

  • Salimo 18:kam
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • Kwa wotsogolera nyimbo. Salimo la mtumiki wa Yehova, Davide, amene anauza Yehova mawu a m’nyimbo iyi pa tsiku limene Yehova anamulanditsa m’manja mwa adani ake onse komanso m’manja mwa Sauli.+ Iye anati:

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena