Ekisodo 15:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndi mulungu wina uti amene angafanane nanu, inu Yehova?+Ndinu woyera kopambana, ndani angafanane ndi inu?+Ndinu woyenera kuopedwa+ ndi kukuimbirani nyimbo zotamanda.+ Inu ndinu wochita zodabwitsa.+ Salimo 92:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ntchito zanu ndi zazikuludi inu Yehova!+Maganizo anu ndi ozama kwambiri.+ Salimo 111:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ntchito za Yehova ndi zazikulu,+ד [Daʹleth]Onse amene amasangalala nazo amazisinkhasinkha.+ Salimo 139:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndidzakutamandani chifukwa munandipanga modabwitsa ndipo zimenezi zimandichititsa mantha.+Ntchito zanu ndi zodabwitsa,+Ndipo ine ndimadziwa bwino zimenezi.+
11 Ndi mulungu wina uti amene angafanane nanu, inu Yehova?+Ndinu woyera kopambana, ndani angafanane ndi inu?+Ndinu woyenera kuopedwa+ ndi kukuimbirani nyimbo zotamanda.+ Inu ndinu wochita zodabwitsa.+
14 Ndidzakutamandani chifukwa munandipanga modabwitsa ndipo zimenezi zimandichititsa mantha.+Ntchito zanu ndi zodabwitsa,+Ndipo ine ndimadziwa bwino zimenezi.+