Salimo 77:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndidzasinkhasinkha za ntchito zanu zonse,+Ndipo ndiziganizira zochita zanu.+ Salimo 92:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pakuti mwandichititsa kusangalala, inu Yehova, chifukwa cha zochita zanu.Ndimafuula mosangalala chifukwa cha ntchito ya manja anu.+ Salimo 143:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndakumbukira masiku akale.+Ndasinkhasinkha zochita zanu zonse,+Ndipo ndakhala ndikuganizira ntchito ya manja anu ndi mtima wonse.+
4 Pakuti mwandichititsa kusangalala, inu Yehova, chifukwa cha zochita zanu.Ndimafuula mosangalala chifukwa cha ntchito ya manja anu.+
5 Ndakumbukira masiku akale.+Ndasinkhasinkha zochita zanu zonse,+Ndipo ndakhala ndikuganizira ntchito ya manja anu ndi mtima wonse.+