1 Mbiri 16:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Muimbireni,+ muimbireni nyimbo zomutamanda!+Sinkhasinkhani ntchito zake zonse zodabwitsa.+ Salimo 105:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Muimbireni, muimbireni nyimbo zomutamanda,+Sinkhasinkhani ntchito zake zonse zodabwitsa.+