Salimo 19:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Zakumwamba zikulengeza ulemerero wa Mulungu.+Ndipo m’mlengalenga mukufotokoza ntchito ya manja ake.+ Salimo 92:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ntchito zanu ndi zazikuludi inu Yehova!+Maganizo anu ndi ozama kwambiri.+ Salimo 104:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ntchito zanu ndi zochuluka, inu Yehova!+Zonsezo munazipanga mwanzeru zanu.+Dziko lapansi ladzaza ndi zinthu zimene munapanga.+ Salimo 111:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ntchito za Yehova ndi zazikulu,+ד [Daʹleth]Onse amene amasangalala nazo amazisinkhasinkha.+
19 Zakumwamba zikulengeza ulemerero wa Mulungu.+Ndipo m’mlengalenga mukufotokoza ntchito ya manja ake.+
24 Ntchito zanu ndi zochuluka, inu Yehova!+Zonsezo munazipanga mwanzeru zanu.+Dziko lapansi ladzaza ndi zinthu zimene munapanga.+