Salimo 15:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Inu Yehova, ndani amene angakhale mlendo m’chihema chanu?+Ndani angakhale m’phiri lanu lopatulika?+ Salimo 140:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndithudi, anthu olungama adzatamanda dzina lanu.+Anthu owongoka mtima adzakhalabe pamaso panu.+ Miyambo 12:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mlomo wa choonadi+ ndi umene udzakhazikike kwamuyaya,+ koma lilime lachinyengo lidzangokhalapo kwa kanthawi.+ Chivumbulutso 21:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako ndinamva mawu ofuula kuchokera kumpando wachifumu, akuti: “Taonani! Chihema+ cha Mulungu chili pakati pa anthu. Iye adzakhala pamodzi nawo,+ ndipo iwo adzakhala anthu ake.+ Zoonadi, Mulunguyo adzakhala nawo.+
15 Inu Yehova, ndani amene angakhale mlendo m’chihema chanu?+Ndani angakhale m’phiri lanu lopatulika?+
19 Mlomo wa choonadi+ ndi umene udzakhazikike kwamuyaya,+ koma lilime lachinyengo lidzangokhalapo kwa kanthawi.+
3 Kenako ndinamva mawu ofuula kuchokera kumpando wachifumu, akuti: “Taonani! Chihema+ cha Mulungu chili pakati pa anthu. Iye adzakhala pamodzi nawo,+ ndipo iwo adzakhala anthu ake.+ Zoonadi, Mulunguyo adzakhala nawo.+