Salimo 32:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Inu olungama, kondwerani chifukwa cha zimene Yehova wachita ndipo sangalalani.+Fuulani ndi chisangalalo inu nonse owongoka mtima.+ Salimo 33:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Fuulani mosangalala chifukwa cha Yehova, inu nonse olungama.+M’poyenera kuti owongoka mtima atamande Mulungu.+
11 Inu olungama, kondwerani chifukwa cha zimene Yehova wachita ndipo sangalalani.+Fuulani ndi chisangalalo inu nonse owongoka mtima.+
33 Fuulani mosangalala chifukwa cha Yehova, inu nonse olungama.+M’poyenera kuti owongoka mtima atamande Mulungu.+