Salimo 68:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma olungama asangalale,+Asekerere pamaso pa Mulungu,+Ndipo akondwere ndi kusangalala.+ Afilipi 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Nthawi zonse kondwerani mwa Ambuye.+ Ndibwerezanso, Kondwerani.+