Deuteronomo 26:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Uzikasangalala+ chifukwa cha zabwino zonse zimene Yehova Mulungu wako wapatsa iwe ndi nyumba yako, zimene wapatsa iweyo komanso Mlevi ndi mlendo wokhala pakati panu.+ Salimo 97:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Sangalalani chifukwa cha Yehova, anthu olungama inu,+Ndipo yamikirani dzina lake loyera.*+ Yesaya 9:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mwachulukitsa mtundu,+ mwaupangitsa kusangalala kwambiri.+ Iwo asangalala pamaso panu ngati mmene amasangalalira pa nthawi yokolola,+ ngati anthu amene amasangalala akamagawana katundu amene alanda.+ 1 Atesalonika 5:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Muzikhala okondwera nthawi zonse.+
11 Uzikasangalala+ chifukwa cha zabwino zonse zimene Yehova Mulungu wako wapatsa iwe ndi nyumba yako, zimene wapatsa iweyo komanso Mlevi ndi mlendo wokhala pakati panu.+
3 Mwachulukitsa mtundu,+ mwaupangitsa kusangalala kwambiri.+ Iwo asangalala pamaso panu ngati mmene amasangalalira pa nthawi yokolola,+ ngati anthu amene amasangalala akamagawana katundu amene alanda.+