Deuteronomo 16:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndipo uzisangalala pa chikondwerero chimenecho,+ iweyo, mwana wako wamwamuna, mwana wako wamkazi, kapolo wako wamwamuna, kapolo wako wamkazi, Mlevi, mlendo wokhala pakati panu, mwana wamasiye ndi mkazi wamasiye, amene ali mumzinda wanu.
14 Ndipo uzisangalala pa chikondwerero chimenecho,+ iweyo, mwana wako wamwamuna, mwana wako wamkazi, kapolo wako wamwamuna, kapolo wako wamkazi, Mlevi, mlendo wokhala pakati panu, mwana wamasiye ndi mkazi wamasiye, amene ali mumzinda wanu.